• globe
    • English
    • Беларуская мова
    • Български
    • Македонски
    • Монгол
    • Русский
    • Українська
    • тоҷикӣ
    • Қазақ тілі
    • Հայերեն
    • עברית
    • العربية
    • بَاسَا سُوْندَا
    • فارسی
    • کوردی
    • 中文 (简体)
    • नेपाली
    • मराठी
    • हिंदी
    • বাংলা
    • ਪੰਜਾਬੀ
    • 日本語
    • Čeština
    • ગુજરાતી
    • తెలుగు
    • ಕನ್ನಡ
    • 繁體中文
    • മലയാളം
    • සිංහල
    • ไทย
    • ພາສາລາວ
    • ကညီလံာ်ခီၣ်ထံး
    • ဗမာစာ
    • ဗမာစာ (Unicode)
    • ქართული
    • አማርኛ
    • 한국어
    • ខេមរភាសា
    • ‫اردو
    • ελληνικά
    • Afrikaans
    • Azərbaycanca
    • Bahasa Melayu
    • Bahasa Melayu Brunei
    • Cрпски
    • Catalŕ
    • ChiShona
    • Cymraeg
    • Dansk
    • Deutsch
    • Eesti
    • Español
    • Filipino
    • Français (Canada)
    • Français (France)
    • Gaeilge
    • Hausa
    • Hmoob
    • Hrvatski
    • Ikirundi
    • Indonesia
    • IsiNdebele
    • isiXhosa
    • isiZulu
    • Italiano
    • Kiswahili
    • Kreyòl ayisyen
    • Latviašu
    • Lietuviškai
    • Luxembourgish
    • Magyar
    • Malagasy
    • Malti
    • Mooré
    • Nederlands
    • Norsk
    • Northern Sotho/Sepedi
    • Oʻzbek
    • Polski
    • Português
    • Română
    • Sesotho sa Borwa
    • Setswana
    • Sinugbuanong Binisaya
    • SiSwati
    • Slovenčina
    • Slovenščina
    • Soomaaliga
    • Srpski
    • Suomi
    • Svenska
    • Türkçe
    • Tagalog
    • Tiếng Việt
    • Venḓa/Tshivenḓa
    • Vlaams
    • Xitsonga
    • Yorůbá
    • Español (European Union)
    • Português (European Union)
    • English (UK)
    • íslenska
    • தமிழ்
    • Bosanski
    • gjuha shqipe
Client Login
Ethics Point - Integrity at Work

Tulani Madandaulo ena kudzera pa EthicsPoint™


 

Chitani Kalondolondo wa Dandaulo lomwe Munadzatula Kale



Kupereka ku mabungwe njira zotulilapo madandaulo mwachinsinsi.

Cholinga cha kampani ya NAVEX ndi kuonetsetsa kuti inu mutha kuyankhula zinthu ndi madandaulo okhudza mchitidwe woyipa komanso wophwanya malamulo pakati pa akuluakulu oyendetsa ntchito za bungwe kapena komiti yaikulu yoyang'anira ntchito za bungwe, ndi kuti mukutha kuyankhula zimenezi motetezeka komanso mwachilungamo popanda inu kudziwika kuti ndinu mwapanga zimenezi.

Kampani ya NAVEX ndiyovomerezeka kuti ili ndi ndondomeko zothana ndi nkhani zokhudza chinsinsi m'maiko a ku Ulaya komanso malamulo ena adziko lapansi, ndipo ili pansi pa Mapulogalamu Oteteza Zinsinsi mumgwirizano wa pakati pa maiko a ku Ulaya ndi dziko la U.S. komanso mumgwirizano wa pakati pa dziko la Switzeland ndi dziko la U.S. kudzera ku Nthambi yoona za Malonda ya United States Department of Commerce.

Timayesetsa kuti ntchito yotula madandaulo kudzera pa EthicsPoint™ ikhale yosavuta komanso yosalira zambiri.. Masamba a paintaneti otsatirawa adzakuthandizani kutula madandaulo munjira yomwe inu simudzadziwika nkomwe. Tsatirani ndondomeko izi kuti mutule madandaulo anu:

  1. Lowetsani dzina la bungwe komwe kwachitikira nkhani yomwe mukufuna kudzatula ndipo sankhani chimodzi cholondola
  2. Dinani pa Mtundu wa Chinyengo womwe ukugwirizana ndi dandaulo lanu
  3. Vomerezani "Ndondomeko Zoyenera Kutsata" kenako lembani nkhani yanu yonse pa fomu
  4. Musanamalize kutula dandaulo lanu, pangani pasiwedi yoti mudzagwiritse ntchito polondoloza za nkhani yomwe mwatulayi.

Mukamaliza kutula dandaulo lanu, mudzapatsidwa nambala ya dandaulo yanu. Pasiwedi ndi nambala ya dandaulo yanu zidzakuthandizani kulondoloza za nkhani yomwe mwatulayi.

NAVEX
Privacy Statement   |  Terms of Use   |  Cookie Statement     
© 2025 NAVEX Global Inc., All Rights Reserved.
TRUSTe
SAS70 Type II